×

oh inu anthu okhulupirira! Musaphwanye kupatulika kwa zizindikiro za Mulungukapenaza MweziWoyera kapenazanyamazimene 5:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:2) ayat 2 in Chichewa

5:2 Surah Al-Ma’idah ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 2 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ لَا تُحِلُّواْ شَعَٰٓئِرَ ٱللَّهِ وَلَا ٱلشَّهۡرَ ٱلۡحَرَامَ وَلَا ٱلۡهَدۡيَ وَلَا ٱلۡقَلَٰٓئِدَ وَلَآ ءَآمِّينَ ٱلۡبَيۡتَ ٱلۡحَرَامَ يَبۡتَغُونَ فَضۡلٗا مِّن رَّبِّهِمۡ وَرِضۡوَٰنٗاۚ وَإِذَا حَلَلۡتُمۡ فَٱصۡطَادُواْۚ وَلَا يَجۡرِمَنَّكُمۡ شَنَـَٔانُ قَوۡمٍ أَن صَدُّوكُمۡ عَنِ ٱلۡمَسۡجِدِ ٱلۡحَرَامِ أَن تَعۡتَدُواْۘ وَتَعَاوَنُواْ عَلَى ٱلۡبِرِّ وَٱلتَّقۡوَىٰۖ وَلَا تَعَاوَنُواْ عَلَى ٱلۡإِثۡمِ وَٱلۡعُدۡوَٰنِۚ وَٱتَّقُواْ ٱللَّهَۖ إِنَّ ٱللَّهَ شَدِيدُ ٱلۡعِقَابِ ﴾
[المَائدة: 2]

oh inu anthu okhulupirira! Musaphwanye kupatulika kwa zizindikiro za Mulungukapenaza MweziWoyera kapenazanyamazimene zimabweretsedwa kukhala nsembe kapena zizindikiro zimene zimaikidwa pa izo kapena za anthu amene amadza ku Nyumba Yoyera kudzafuna chisomo ndi chisangalalo cha Ambuye wawo. Koma mukatsiriza miyambo ya Hajji, mukhoza kusaka ndipo musalole chidani cha anthu ena amene anakuletsani kulowa mu Mzikiti Woyera kuti chikuchimwitseni. Thandizanani wina ndi mnzake pa ntchito zabwino koma musathandizane mu ntchito ya uchimo ndi yoswa malamulo. Muopeni Mulungu. Ndithudi Mulungu amalanga kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها الذين آمنوا لا تحلوا شعائر الله ولا الشهر الحرام ولا الهدي, باللغة نيانجا

﴿ياأيها الذين آمنوا لا تحلوا شعائر الله ولا الشهر الحرام ولا الهدي﴾ [المَائدة: 2]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek