×

Ndipo atatero Mulungu adatumiza khwangwala amene adakumba pansi ndi kumulangiza mmene iye 5:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:31) ayat 31 in Chichewa

5:31 Surah Al-Ma’idah ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 31 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿فَبَعَثَ ٱللَّهُ غُرَابٗا يَبۡحَثُ فِي ٱلۡأَرۡضِ لِيُرِيَهُۥ كَيۡفَ يُوَٰرِي سَوۡءَةَ أَخِيهِۚ قَالَ يَٰوَيۡلَتَىٰٓ أَعَجَزۡتُ أَنۡ أَكُونَ مِثۡلَ هَٰذَا ٱلۡغُرَابِ فَأُوَٰرِيَ سَوۡءَةَ أَخِيۖ فَأَصۡبَحَ مِنَ ٱلنَّٰدِمِينَ ﴾
[المَائدة: 31]

Ndipo atatero Mulungu adatumiza khwangwala amene adakumba pansi ndi kumulangiza mmene iye angakwiririre mtembo wa m’bale wake. Iye adati: “Kalanga ine! Ndalephera kukhala ngati khwangwala uyu ndi kukwirira mtembo wa m’bale wanga?” Ndipo iye adali mmodzi wa anthu onong’oneza bombono

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فبعث الله غرابا يبحث في الأرض ليريه كيف يواري سوأة أخيه قال, باللغة نيانجا

﴿فبعث الله غرابا يبحث في الأرض ليريه كيف يواري سوأة أخيه قال﴾ [المَائدة: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Pamenepo Allah adatumiza khwangwala yemwe amafukula pansi kuti amusonyeze mmene angakwililire mtembo wa m’bale wake. (Wopha mnzake) adati: “Kalanga ine! Ndalephera kuti ndifanane ndi khwangwala uyu, kuti ndikwilire mtembo wa m’bale wanga.” Choncho adali mmodzi mwa odzinena
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek