×

Messiya, mwana wamwamuna wa Maria, sadali wina aliyense ayi koma Mtumwi, Atumwi 5:75 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:75) ayat 75 in Chichewa

5:75 Surah Al-Ma’idah ayat 75 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 75 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿مَّا ٱلۡمَسِيحُ ٱبۡنُ مَرۡيَمَ إِلَّا رَسُولٞ قَدۡ خَلَتۡ مِن قَبۡلِهِ ٱلرُّسُلُ وَأُمُّهُۥ صِدِّيقَةٞۖ كَانَا يَأۡكُلَانِ ٱلطَّعَامَۗ ٱنظُرۡ كَيۡفَ نُبَيِّنُ لَهُمُ ٱلۡأٓيَٰتِ ثُمَّ ٱنظُرۡ أَنَّىٰ يُؤۡفَكُونَ ﴾
[المَائدة: 75]

Messiya, mwana wamwamuna wa Maria, sadali wina aliyense ayi koma Mtumwi, Atumwi ena adadza iye asadadze. Mayi wake adali mayi wokhulupilira. onse adali kudya chakudya. Taona mmene timaonetsera kwa iwo poyera chivumbulutso chathu ndipo taona mmene iwo amatembenuzira choonadi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ما المسيح ابن مريم إلا رسول قد خلت من قبله الرسل وأمه, باللغة نيانجا

﴿ما المسيح ابن مريم إلا رسول قد خلت من قبله الرسل وأمه﴾ [المَائدة: 75]

Khaled Ibrahim Betala
“Mesiya mwana wa Mariya sali chilichonse koma ndi Mtumiki wa Allah chabe. Ndithudi, atumiki ambiri adapita kale patsogolo pake. Nayenso mayi wake ndi mkazi wachoonadi, onse awiri adali kudya chakudya, (ndipo chotsatira chake amapita kokadzithandiza. Nanga ndi milungu yotani yopita kukadzithandiza?) Taona momwe tikufotokozera kwa iwo zizindikiro. Taonanso mmene akutembenuziridwa (kusiya choonadi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek