×

Nena: “Kodi inu muzipembedza, powonjezera pa Mulungu, chinthu chimene sichingathe kukuonongani kapena 5:76 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ma’idah ⮕ (5:76) ayat 76 in Chichewa

5:76 Surah Al-Ma’idah ayat 76 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ma’idah ayat 76 - المَائدة - Page - Juz 6

﴿قُلۡ أَتَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَا لَا يَمۡلِكُ لَكُمۡ ضَرّٗا وَلَا نَفۡعٗاۚ وَٱللَّهُ هُوَ ٱلسَّمِيعُ ٱلۡعَلِيمُ ﴾
[المَائدة: 76]

Nena: “Kodi inu muzipembedza, powonjezera pa Mulungu, chinthu chimene sichingathe kukuonongani kapena kukuthandizani?” Koma Mulungu ndiye amamva zonse ndiponso amadziwa zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل أتعبدون من دون الله ما لا يملك لكم ضرا ولا نفعا, باللغة نيانجا

﴿قل أتعبدون من دون الله ما لا يملك لكم ضرا ولا نفعا﴾ [المَائدة: 76]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Kodi mukupembedza chimene sichingakupatseni vuto ngakhale chabwino, kusiya Allah? Pomwe Allah ndiye Wakumva, Wodziwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek