×

Ndipo, ndithudi, iwo adafuna kuchititsa manyazi alendo ake. Motero Ife tidawachititsa khungu. 54:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qamar ⮕ (54:37) ayat 37 in Chichewa

54:37 Surah Al-Qamar ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qamar ayat 37 - القَمَر - Page - Juz 27

﴿وَلَقَدۡ رَٰوَدُوهُ عَن ضَيۡفِهِۦ فَطَمَسۡنَآ أَعۡيُنَهُمۡ فَذُوقُواْ عَذَابِي وَنُذُرِ ﴾
[القَمَر: 37]

Ndipo, ndithudi, iwo adafuna kuchititsa manyazi alendo ake. Motero Ife tidawachititsa khungu. Kotero inu lawani chilango changa ndi machenjezo anga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد راودوه عن ضيفه فطمسنا أعينهم فذوقوا عذابي ونذر, باللغة نيانجا

﴿ولقد راودوه عن ضيفه فطمسنا أعينهم فذوقوا عذابي ونذر﴾ [القَمَر: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu adafuna kwa iye kuti awapatse alendo ake (kuti achite nawo zauve), koma tidafafaniza maso awo (kuti ikhale mphoto pa zimene adafunazo). (Ndipo tidawauza): “Choncho lawani chilango Changa ndi machenjezo Anga.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek