Quran with Chichewa translation - Surah Al-Waqi‘ah ayat 18 - الوَاقِعة - Page - Juz 27
﴿بِأَكۡوَابٖ وَأَبَارِيقَ وَكَأۡسٖ مِّن مَّعِينٖ ﴾
[الوَاقِعة: 18]
﴿بأكواب وأباريق وكأس من معين﴾ [الوَاقِعة: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Uku atatenga matambula ndi maketulo (odzaza ndi zakumwa za ku Jannah), ndi zipanda zodzaza ndi zakumwa zochokera mu akasupe oyenda |