×

Kodi ndi chifukwa chiyani inu simufuna kupereka m’njira ya Mulungu? Mulungu ndiye 57:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:10) ayat 10 in Chichewa

57:10 Surah Al-hadid ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 10 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿وَمَا لَكُمۡ أَلَّا تُنفِقُواْ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ وَلِلَّهِ مِيرَٰثُ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ لَا يَسۡتَوِي مِنكُم مَّنۡ أَنفَقَ مِن قَبۡلِ ٱلۡفَتۡحِ وَقَٰتَلَۚ أُوْلَٰٓئِكَ أَعۡظَمُ دَرَجَةٗ مِّنَ ٱلَّذِينَ أَنفَقُواْ مِنۢ بَعۡدُ وَقَٰتَلُواْۚ وَكُلّٗا وَعَدَ ٱللَّهُ ٱلۡحُسۡنَىٰۚ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ خَبِيرٞ ﴾
[الحدِيد: 10]

Kodi ndi chifukwa chiyani inu simufuna kupereka m’njira ya Mulungu? Mulungu ndiye Mwini wa zonse zili kumwamba ndi padziko lapansi. Palibe ofanana, pakati panu, ndi iwo amene amapereka chaulere ndipo adamenya nawo nkhondo poyamba kupambana kusanadze. Amenewa ndi a pamwamba kuposa iwo amene adapereka chaulere ndi kumenya nkhondo pambuyo pake. Koma kwa onsewa, Mulungu walonjeza mphotho yokoma. Ndipo Mulungu amadziwa zonse zimene mumachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما لكم ألا تنفقوا في سبيل الله ولله ميراث السموات والأرض لا, باللغة نيانجا

﴿وما لكم ألا تنفقوا في سبيل الله ولله ميراث السموات والأرض لا﴾ [الحدِيد: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi ndichifukwa chiani simukupereka pa njira ya Allah (chuma chanu) pamene Allah Ndimwini wa zosiyidwa zonse za kumwamba ndi za m’dziko lapansi. Sali ofanana mwa inu amene adapereka chuma (panjira ya Allah) pamodzi ndi kumenya nkhondo usadagonjetsedwe (mzinda wa Makka), iwowo ndiomwe ali ndi ulemelero waukulu kuposa amene apereka chuma chawo ndi kumenya nkhondo pambuyo. Koma onsewo Allah wawalonjeza zabwino (ngakhale ali osiyana ulemelero wawo); ndipo Allah akudziwa zonse zimene muchita. (Choncho aliyense adzalipidwa molingana ndi zimene amachita)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek