×

Dziwani kuti Mulungu amapereka moyo ku nthaka ikafa. Ndithudi taonetsa chivumbulutso chathu 57:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hadid ⮕ (57:17) ayat 17 in Chichewa

57:17 Surah Al-hadid ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hadid ayat 17 - الحدِيد - Page - Juz 27

﴿ٱعۡلَمُوٓاْ أَنَّ ٱللَّهَ يُحۡيِ ٱلۡأَرۡضَ بَعۡدَ مَوۡتِهَاۚ قَدۡ بَيَّنَّا لَكُمُ ٱلۡأٓيَٰتِ لَعَلَّكُمۡ تَعۡقِلُونَ ﴾
[الحدِيد: 17]

Dziwani kuti Mulungu amapereka moyo ku nthaka ikafa. Ndithudi taonetsa chivumbulutso chathu poyera kwa inu kuti mukhoza kuzindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: اعلموا أن الله يحيي الأرض بعد موتها قد بينا لكم الآيات لعلكم, باللغة نيانجا

﴿اعلموا أن الله يحيي الأرض بعد موتها قد بينا لكم الآيات لعلكم﴾ [الحدِيد: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Dziwani kuti ndithu Allah amaukitsa nthaka itauma (poitsitsira mvula kuti mmera umere). Choncho takulongosolerani zisonyezo kuti inu mukhale ndi nzeru
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek