Quran with Chichewa translation - Surah Al-hashr ayat 23 - الحَشر - Page - Juz 28
﴿هُوَ ٱللَّهُ ٱلَّذِي لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَ ٱلۡمَلِكُ ٱلۡقُدُّوسُ ٱلسَّلَٰمُ ٱلۡمُؤۡمِنُ ٱلۡمُهَيۡمِنُ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡجَبَّارُ ٱلۡمُتَكَبِّرُۚ سُبۡحَٰنَ ٱللَّهِ عَمَّا يُشۡرِكُونَ ﴾
[الحَشر: 23]
﴿هو الله الذي لا إله إلا هو الملك القدوس السلام المؤمن المهيمن﴾ [الحَشر: 23]
Khaled Ibrahim Betala “Iye ndi Allah, Amene palibenso wina wopembedzedwa mwachoonadi koma Iye, Mfumu, Woyera, Mwini mtendere, Wotsimikizira (aneneri Ake mphamvu yochitira zozizwitsa,) Msungi wa chilichonse (yemwe akuona zochita za akapolo Ake;) Wamphamvu zopambana, Mgonjetsi Wotukuka muulemelero; Wamkulukulu. Wayeretsedwa Allah kuzimene akumuphatikiza nazo |