×

Motero Ife timafotokoza chivumbulutso chathu, kuti iwo anene kuti: “Iwe waphunzira” ndi 6:105 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-An‘am ⮕ (6:105) ayat 105 in Chichewa

6:105 Surah Al-An‘am ayat 105 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 105 - الأنعَام - Page - Juz 7

﴿وَكَذَٰلِكَ نُصَرِّفُ ٱلۡأٓيَٰتِ وَلِيَقُولُواْ دَرَسۡتَ وَلِنُبَيِّنَهُۥ لِقَوۡمٖ يَعۡلَمُونَ ﴾
[الأنعَام: 105]

Motero Ife timafotokoza chivumbulutso chathu, kuti iwo anene kuti: “Iwe waphunzira” ndi kuti tifotokoze momveka kwa anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وكذلك نصرف الآيات وليقولوا درست ولنبينه لقوم يعلمون, باللغة نيانجا

﴿وكذلك نصرف الآيات وليقولوا درست ولنبينه لقوم يعلمون﴾ [الأنعَام: 105]

Khaled Ibrahim Betala
“Motero tikulongosola mwatsatanetsatane zizindikiro, (kuti azindikire). Ndikuti anene: “Wachita kuphunzira (izi, si Allah amene wakuuza.” Ndipo tazibwerezabwereza chonchi) kuti tilongosole ndi kufotokoza momveka kwa anthu odziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek