Quran with Chichewa translation - Surah Al-An‘am ayat 83 - الأنعَام - Page - Juz 7
﴿وَتِلۡكَ حُجَّتُنَآ ءَاتَيۡنَٰهَآ إِبۡرَٰهِيمَ عَلَىٰ قَوۡمِهِۦۚ نَرۡفَعُ دَرَجَٰتٖ مَّن نَّشَآءُۗ إِنَّ رَبَّكَ حَكِيمٌ عَلِيمٞ ﴾
[الأنعَام: 83]
﴿وتلك حجتنا آتيناها إبراهيم على قومه نرفع درجات من نشاء إن ربك﴾ [الأنعَام: 83]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo izi ndi zizindikiro Zathu (mitsutso Yathu), zomwe tidampatsa Ibrahim pa anthu ake. Timamtukulira ulemelero amene tamfuna. Ndithu Mbuye wako Ngwanzeru zakuya, Ngodziwa kwambiri |