×

Ngati iwo akupambanani, ndithudi, adzakuonetsani kuti ndi adani anu ndipo adzagwiritsa ntchito 60:2 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:2) ayat 2 in Chichewa

60:2 Surah Al-Mumtahanah ayat 2 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 2 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿إِن يَثۡقَفُوكُمۡ يَكُونُواْ لَكُمۡ أَعۡدَآءٗ وَيَبۡسُطُوٓاْ إِلَيۡكُمۡ أَيۡدِيَهُمۡ وَأَلۡسِنَتَهُم بِٱلسُّوٓءِ وَوَدُّواْ لَوۡ تَكۡفُرُونَ ﴾
[المُمتَحنَة: 2]

Ngati iwo akupambanani, ndithudi, adzakuonetsani kuti ndi adani anu ndipo adzagwiritsa ntchito manja awo ndi malirime awo pa inu pokuchitirani zoipa. Iwo afunitsitsa kuti nanu mukhale anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن يثقفوكم يكونوا لكم أعداء ويبسطوا إليكم أيديهم وألسنتهم بالسوء وودوا لو, باللغة نيانجا

﴿إن يثقفوكم يكونوا لكم أعداء ويبسطوا إليكم أيديهم وألسنتهم بالسوء وودوا لو﴾ [المُمتَحنَة: 2]

Khaled Ibrahim Betala
“Akakumana nanu (pankhondo) akukhala adani anu ndipo akukutambasulirani manja ndi malirime awo moipa (pokumenyani ndi kukutukwanani); ndipo akulakalaka mukadakhala osakhulupirira (kuti mufanane nawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek