×

Mwina Mulungu angakhazikitse chikondi pakati pa inu ndi iwo amene inu mumawaganizira 60:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:7) ayat 7 in Chichewa

60:7 Surah Al-Mumtahanah ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 7 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿۞ عَسَى ٱللَّهُ أَن يَجۡعَلَ بَيۡنَكُمۡ وَبَيۡنَ ٱلَّذِينَ عَادَيۡتُم مِّنۡهُم مَّوَدَّةٗۚ وَٱللَّهُ قَدِيرٞۚ وَٱللَّهُ غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[المُمتَحنَة: 7]

Mwina Mulungu angakhazikitse chikondi pakati pa inu ndi iwo amene inu mumawaganizira kuti ndi adani anu. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu pa china chilichonse ndipo Mulungu ndi wokhululukira ndi Mwini chisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: عسى الله أن يجعل بينكم وبين الذين عاديتم منهم مودة والله قدير, باللغة نيانجا

﴿عسى الله أن يجعل بينكم وبين الذين عاديتم منهم مودة والله قدير﴾ [المُمتَحنَة: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“Mwina Allah angaike chikondi pakati panu ndi ena mwa amene mumawada (poiongolera mitima yawo kukhulupirira mwa Allah), ndipo Allah Ngokhoza chilichonse ndiponso Allah Ngokhululuka; Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek