×

Mulungu sali kukuletsani kuti muonetse chilungamo ndi chisoni kwa iwo amene sadamenyane 60:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mumtahanah ⮕ (60:8) ayat 8 in Chichewa

60:8 Surah Al-Mumtahanah ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mumtahanah ayat 8 - المُمتَحنَة - Page - Juz 28

﴿لَّا يَنۡهَىٰكُمُ ٱللَّهُ عَنِ ٱلَّذِينَ لَمۡ يُقَٰتِلُوكُمۡ فِي ٱلدِّينِ وَلَمۡ يُخۡرِجُوكُم مِّن دِيَٰرِكُمۡ أَن تَبَرُّوهُمۡ وَتُقۡسِطُوٓاْ إِلَيۡهِمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ يُحِبُّ ٱلۡمُقۡسِطِينَ ﴾
[المُمتَحنَة: 8]

Mulungu sali kukuletsani kuti muonetse chilungamo ndi chisoni kwa iwo amene sadamenyane nanu chifukwa cha chikhulupiliro chanu ndipo sanakuthamangitseni mu nyumba zanu. Ndithudi, Mulungu amakonda iwo amene amachita zolungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لا ينهاكم الله عن الذين لم يقاتلوكم في الدين ولم يخرجوكم من, باللغة نيانجا

﴿لا ينهاكم الله عن الذين لم يقاتلوكم في الدين ولم يخرجوكم من﴾ [المُمتَحنَة: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“Allah sakukuletsani kuwachitira zabwino ndi chilungamo amene sadakumenyeni ndi kukutulutsani m’nyumba zanu chifukwa cha chipembedzo. Ndithu Allah amakonda achilungamo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek