×

Kuti mukhulupirire mwa Mulungu ndi mwa Mtumwi wake, kuti mudzipereke kwathunthu mu 61:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saff ⮕ (61:11) ayat 11 in Chichewa

61:11 Surah As-saff ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saff ayat 11 - الصَّف - Page - Juz 28

﴿تُؤۡمِنُونَ بِٱللَّهِ وَرَسُولِهِۦ وَتُجَٰهِدُونَ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ بِأَمۡوَٰلِكُمۡ وَأَنفُسِكُمۡۚ ذَٰلِكُمۡ خَيۡرٞ لَّكُمۡ إِن كُنتُمۡ تَعۡلَمُونَ ﴾
[الصَّف: 11]

Kuti mukhulupirire mwa Mulungu ndi mwa Mtumwi wake, kuti mudzipereke kwathunthu mu njira ya Mulungu pogwiritsa ntchito chuma chanu ndi inu eni ake. Chimenechi ndicho chinthu chabwino kwa inu ngati inu mukadadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: تؤمنون بالله ورسوله وتجاهدون في سبيل الله بأموالكم وأنفسكم ذلكم خير لكم, باللغة نيانجا

﴿تؤمنون بالله ورسوله وتجاهدون في سبيل الله بأموالكم وأنفسكم ذلكم خير لكم﴾ [الصَّف: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Muzimkhulupirira Allah ndi Mtumiki Wake; ndipo muzichita Jihâd pa njira ya Allah ndi chuma chanu, ndi matupi anu. Zimenezo nzabwino kwa inu ngati muli odziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek