×

Iyeadzakukhululukiraniinumachimoanu ndi kukulandirani m’minda imene pansi pake pamayenda mitsinje, ndipo adzakulowetsani m’nyumba 61:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-saff ⮕ (61:12) ayat 12 in Chichewa

61:12 Surah As-saff ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-saff ayat 12 - الصَّف - Page - Juz 28

﴿يَغۡفِرۡ لَكُمۡ ذُنُوبَكُمۡ وَيُدۡخِلۡكُمۡ جَنَّٰتٖ تَجۡرِي مِن تَحۡتِهَا ٱلۡأَنۡهَٰرُ وَمَسَٰكِنَ طَيِّبَةٗ فِي جَنَّٰتِ عَدۡنٖۚ ذَٰلِكَ ٱلۡفَوۡزُ ٱلۡعَظِيمُ ﴾
[الصَّف: 12]

Iyeadzakukhululukiraniinumachimoanu ndi kukulandirani m’minda imene pansi pake pamayenda mitsinje, ndipo adzakulowetsani m’nyumba zokongola ndi zaulemu za m’Paradiso. Kumeneko, ndithudi, ndiko kupambana kwenikweni

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يغفر لكم ذنوبكم ويدخلكم جنات تجري من تحتها الأنهار ومساكن طيبة في, باللغة نيانجا

﴿يغفر لكم ذنوبكم ويدخلكم جنات تجري من تحتها الأنهار ومساكن طيبة في﴾ [الصَّف: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“Akukhululukirani machimo anu ndipo akulowetsani m’minda momwe mitsinje ikuyenda pansi pake, ndiponso (adzakupatsani) mokhala mwabwino ku minda yamuyaya. Kumeneko ndiko kupambana kwakukulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek