Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jumu‘ah ayat 3 - الجُمعَة - Page - Juz 28
﴿وَءَاخَرِينَ مِنۡهُمۡ لَمَّا يَلۡحَقُواْ بِهِمۡۚ وَهُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[الجُمعَة: 3]
﴿وآخرين منهم لما يلحقوا بهم وهو العزيز الحكيم﴾ [الجُمعَة: 3]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (adamtumizanso) kwa ena mwa iwo, omwe sadakumane nawo, ndipo Iye (Allah) Ngopambana (pa chinthu chilichonse ndi Wamphamvu zoposa ndiponso) Ngwanzeru zakuya |