Quran with Chichewa translation - Surah Al-Jumu‘ah ayat 4 - الجُمعَة - Page - Juz 28
﴿ذَٰلِكَ فَضۡلُ ٱللَّهِ يُؤۡتِيهِ مَن يَشَآءُۚ وَٱللَّهُ ذُو ٱلۡفَضۡلِ ٱلۡعَظِيمِ ﴾
[الجُمعَة: 4]
﴿ذلك فضل الله يؤتيه من يشاء والله ذو الفضل العظيم﴾ [الجُمعَة: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Umenewo ndiwo ubwino wa Allah akuupereka kwa amene wamfuna (mwa akapolo Ake); ndipo Allah yekha ndi Mwini ubwino waukulu |