×

oh iwe Mtumwi! Limbika kwambiri pogonjetsa anthu osakhulupirira ndi anthu a chinyengo 66:9 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Tahrim ⮕ (66:9) ayat 9 in Chichewa

66:9 Surah At-Tahrim ayat 9 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Tahrim ayat 9 - التَّحرِيم - Page - Juz 28

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّبِيُّ جَٰهِدِ ٱلۡكُفَّارَ وَٱلۡمُنَٰفِقِينَ وَٱغۡلُظۡ عَلَيۡهِمۡۚ وَمَأۡوَىٰهُمۡ جَهَنَّمُۖ وَبِئۡسَ ٱلۡمَصِيرُ ﴾
[التَّحرِيم: 9]

oh iwe Mtumwi! Limbika kwambiri pogonjetsa anthu osakhulupirira ndi anthu a chinyengo ndipo chita nawo mwankhanza, malo awo ndi kumoto, omwe ndi malo oipa kwambiri kukhalako

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها النبي جاهد الكفار والمنافقين واغلظ عليهم ومأواهم جهنم وبئس المصير, باللغة نيانجا

﴿ياأيها النبي جاهد الكفار والمنافقين واغلظ عليهم ومأواهم جهنم وبئس المصير﴾ [التَّحرِيم: 9]

Khaled Ibrahim Betala
“E iwe Mneneri! Limbana ndi akafiri (osakhulupirira) ndi Amunafikina (Achiphamaso), aumire mtima. Ndipo malo awo ndi ku Jahannam, taonani kuipa kobwerera (kwawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek