Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 14 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿قَالَ أَنظِرۡنِيٓ إِلَىٰ يَوۡمِ يُبۡعَثُونَ ﴾
[الأعرَاف: 14]
﴿قال أنظرني إلى يوم يبعثون﴾ [الأعرَاف: 14]
Khaled Ibrahim Betala “(Satana) adati: “Ndipatseni nthawi mpaka tsiku limene adzaukitsidwa (akapolo anu ku imfa).” |