×

Mulungu adati: “Choka kumene kuno. Ano simalo okhalako munthu wa mtudzu ayi. 7:13 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:13) ayat 13 in Chichewa

7:13 Surah Al-A‘raf ayat 13 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 13 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿قَالَ فَٱهۡبِطۡ مِنۡهَا فَمَا يَكُونُ لَكَ أَن تَتَكَبَّرَ فِيهَا فَٱخۡرُجۡ إِنَّكَ مِنَ ٱلصَّٰغِرِينَ ﴾
[الأعرَاف: 13]

Mulungu adati: “Choka kumene kuno. Ano simalo okhalako munthu wa mtudzu ayi. Choka! Chifukwa iwe ndiwe mmodzi wa anthu onyozedwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال فاهبط منها فما يكون لك أن تتكبر فيها فاخرج إنك من, باللغة نيانجا

﴿قال فاهبط منها فما يكون لك أن تتكبر فيها فاخرج إنك من﴾ [الأعرَاف: 13]

Khaled Ibrahim Betala
“(Allah) adati: “Choncho, choka m’menemo ndi kutsikira pansi. Sikofunika kwa iwe kudzitama m’menemo. Tuluka, ndithu iwe ndiwe mmodzi wa onyozeka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek