×

Kapena mwina mungadzanene kuti, “Ndi makolo athu akale amene amapembedza milungu ina 7:173 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:173) ayat 173 in Chichewa

7:173 Surah Al-A‘raf ayat 173 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 173 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿أَوۡ تَقُولُوٓاْ إِنَّمَآ أَشۡرَكَ ءَابَآؤُنَا مِن قَبۡلُ وَكُنَّا ذُرِّيَّةٗ مِّنۢ بَعۡدِهِمۡۖ أَفَتُهۡلِكُنَا بِمَا فَعَلَ ٱلۡمُبۡطِلُونَ ﴾
[الأعرَاف: 173]

Kapena mwina mungadzanene kuti, “Ndi makolo athu akale amene amapembedza milungu ina pambali pa Mulungu. Ife tidali m’badwo wapambuyo pawo. Kodi inu mutiononga chifukwa cha zimene adachita anthu oipa?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو تقولوا إنما أشرك آباؤنا من قبل وكنا ذرية من بعدهم أفتهلكنا, باللغة نيانجا

﴿أو تقولوا إنما أشرك آباؤنا من قبل وكنا ذرية من بعدهم أفتهلكنا﴾ [الأعرَاف: 173]

Khaled Ibrahim Betala
“Kapena mungadzati: “Makolo athu ndi amene adapembedza mafano kale, ndipo ife tidali ana odza pambuyo pawo (choncho tidawatsatira pazimene ankachita). Kodi nanga mutiononga chifukwa cha zomwe adachita oipa?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek