×

Ndithudi iwo amene mumawapembedza powonjezera pa Mulungu weniweni ndi akapolo ngati inu 7:194 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:194) ayat 194 in Chichewa

7:194 Surah Al-A‘raf ayat 194 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 194 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ تَدۡعُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ عِبَادٌ أَمۡثَالُكُمۡۖ فَٱدۡعُوهُمۡ فَلۡيَسۡتَجِيبُواْ لَكُمۡ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[الأعرَاف: 194]

Ndithudi iwo amene mumawapembedza powonjezera pa Mulungu weniweni ndi akapolo ngati inu nomwe. Motero aitaneni ndipo akuyankheni ngati zimene munena ndi zoonadi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين تدعون من دون الله عباد أمثالكم فادعوهم فليستجيبوا لكم إن, باللغة نيانجا

﴿إن الذين تدعون من دون الله عباد أمثالكم فادعوهم فليستجيبوا لكم إن﴾ [الأعرَاف: 194]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene mukuwapembedza kusiya Allah, ndi akapolo monga inu. (Koma inu muposa iwo). Choncho aitaneni ndipo akuyankheni ngati inu mulidi owona (pa zimene mukunenazi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek