×

Kodi iwo ali ndi miyendo yoti angayendere? Kodi ali ndi manja oti 7:195 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:195) ayat 195 in Chichewa

7:195 Surah Al-A‘raf ayat 195 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 195 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿أَلَهُمۡ أَرۡجُلٞ يَمۡشُونَ بِهَآۖ أَمۡ لَهُمۡ أَيۡدٖ يَبۡطِشُونَ بِهَآۖ أَمۡ لَهُمۡ أَعۡيُنٞ يُبۡصِرُونَ بِهَآۖ أَمۡ لَهُمۡ ءَاذَانٞ يَسۡمَعُونَ بِهَاۗ قُلِ ٱدۡعُواْ شُرَكَآءَكُمۡ ثُمَّ كِيدُونِ فَلَا تُنظِرُونِ ﴾
[الأعرَاف: 195]

Kodi iwo ali ndi miyendo yoti angayendere? Kodi ali ndi manja oti angagwire china chilichonse? Kapena ali ndi maso oti angaonere? Kapena ali ndi makutu oti angamvere? Nena, “Itanani milungu yanu yabodza ndipo pangani chiwembu chanu pa ine ndipo musandipatse mpumulo ayi.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألهم أرجل يمشون بها أم لهم أيد يبطشون بها أم لهم أعين, باللغة نيانجا

﴿ألهم أرجل يمشون بها أم لهم أيد يبطشون بها أم لهم أعين﴾ [الأعرَاف: 195]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi iwo ali nayo miyendo yoyendera? Kapena ali nawo manja ogwilira. Kapena ali nawo maso openyera? Kapena ali nawo makutu omvelera? Nena: “Aitaneni aphatikizi anuwo, ndipo kenako ndichitireni chiwembu ndipo musandipatse nthawi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek