×

Oh inu ana a Adamu! Ife takupatsani zovala kuti mubise umaliseche wanu 7:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:26) ayat 26 in Chichewa

7:26 Surah Al-A‘raf ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 26 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿يَٰبَنِيٓ ءَادَمَ قَدۡ أَنزَلۡنَا عَلَيۡكُمۡ لِبَاسٗا يُوَٰرِي سَوۡءَٰتِكُمۡ وَرِيشٗاۖ وَلِبَاسُ ٱلتَّقۡوَىٰ ذَٰلِكَ خَيۡرٞۚ ذَٰلِكَ مِنۡ ءَايَٰتِ ٱللَّهِ لَعَلَّهُمۡ يَذَّكَّرُونَ ﴾
[الأعرَاف: 26]

Oh inu ana a Adamu! Ife takupatsani zovala kuti mubise umaliseche wanu ndi zovala zokukongoletsani ndi chobvala cha chilungamo chimene chili chabwino. Zimenezo ndi zina mwa zizindikiro za Mulungu kuti akhale okumbuka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يابني آدم قد أنـزلنا عليكم لباسا يواري سوآتكم وريشا ولباس التقوى ذلك, باللغة نيانجا

﴿يابني آدم قد أنـزلنا عليكم لباسا يواري سوآتكم وريشا ولباس التقوى ذلك﴾ [الأعرَاف: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“E inu ana a Adam! Ndithu tatsitsa kwa inu chovala chobisa umaliseche wanu ndi chodzikongoletsera nacho. Koma chovala choopa nacho Allah (pakudziyeretsa ku zoletsedwa) chimenecho ndicho chabwino koposa. Zimenezo ndi zizindikiro za (chisomo cha) Allah kuti iwo akumbukire
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek