Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 25 - الأعرَاف - Page - Juz 8
﴿قَالَ فِيهَا تَحۡيَوۡنَ وَفِيهَا تَمُوتُونَ وَمِنۡهَا تُخۡرَجُونَ ﴾
[الأعرَاف: 25]
﴿قال فيها تحيون وفيها تموتون ومنها تخرجون﴾ [الأعرَاف: 25]
Khaled Ibrahim Betala “(Allah) adatinso: “Muzikakhala moyo pamenepo, ndipo muzikafa pamenepo; ndipo momwemo mudzatulutsidwa (mutauka kwa akufa).” |