×

Ndithudi Ambuye wanu ndi Mulungu, amene m’masiku asanu ndi limodzi adalenga kumwamba 7:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:54) ayat 54 in Chichewa

7:54 Surah Al-A‘raf ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 54 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿إِنَّ رَبَّكُمُ ٱللَّهُ ٱلَّذِي خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ فِي سِتَّةِ أَيَّامٖ ثُمَّ ٱسۡتَوَىٰ عَلَى ٱلۡعَرۡشِۖ يُغۡشِي ٱلَّيۡلَ ٱلنَّهَارَ يَطۡلُبُهُۥ حَثِيثٗا وَٱلشَّمۡسَ وَٱلۡقَمَرَ وَٱلنُّجُومَ مُسَخَّرَٰتِۭ بِأَمۡرِهِۦٓۗ أَلَا لَهُ ٱلۡخَلۡقُ وَٱلۡأَمۡرُۗ تَبَارَكَ ٱللَّهُ رَبُّ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[الأعرَاف: 54]

Ndithudi Ambuye wanu ndi Mulungu, amene m’masiku asanu ndi limodzi adalenga kumwamba ndi dziko lapansi ndipo atatero adabuka pamwamba pa Mpando wake wa Chifumu. Iye amavundikira usiku ndi usana ndipo mofulumira usiku umatsata usana. Ndipo dzuwa, mwezi ndi nyenyezi zimayenda motsatira malamulo ake. Ndithudi zake ndi zolengedwa zonse ndi ulamuliro. Olemekezeka akhale Mulungu, Ambuye wa zolengedwa zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن ربكم الله الذي خلق السموات والأرض في ستة أيام ثم استوى, باللغة نيانجا

﴿إن ربكم الله الذي خلق السموات والأرض في ستة أيام ثم استوى﴾ [الأعرَاف: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, Mbuye wanu ndi Allah Yemwe adalenga thambo ndi nthaka m’masiku asanu ndi limodzi. Kenako adakhazikika pa Arsh (Mpando Wake wachifumu). Amauchita usiku kuti uvindikire usana, zimatsatana mwamsangamsanga. Ndipo dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi nzofewetsedwa, (zikuyenda mogonjera) ndi Lamulo Lake. Dziwani kuti kulenga ndi kulamula Nkwake. Ndithudi, watukuka Allah Mbuye Wazolengedwa (zonse)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek