×

Ife tidamupulumutsa iye ndi onse amene adali naye mwa chifundo chathu ndipo 7:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:72) ayat 72 in Chichewa

7:72 Surah Al-A‘raf ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 72 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿فَأَنجَيۡنَٰهُ وَٱلَّذِينَ مَعَهُۥ بِرَحۡمَةٖ مِّنَّا وَقَطَعۡنَا دَابِرَ ٱلَّذِينَ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِنَاۖ وَمَا كَانُواْ مُؤۡمِنِينَ ﴾
[الأعرَاف: 72]

Ife tidamupulumutsa iye ndi onse amene adali naye mwa chifundo chathu ndipo tidadula maziko ya onse amene anatsutsa chivumbulutso chathu ndipo iwo adali osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأنجيناه والذين معه برحمة منا وقطعنا دابر الذين كذبوا بآياتنا وما كانوا, باللغة نيانجا

﴿فأنجيناه والذين معه برحمة منا وقطعنا دابر الذين كذبوا بآياتنا وما كانوا﴾ [الأعرَاف: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho tidampulumutsa pamodzi ndi amene adali naye mwa chifundo chathu, ndipo tidadula mizu ya omwe adatsutsa zivumbulutso Zathu. Ndipo sadali okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek