×

Ndipo kwa anthu a Thamud, Ife tidawatumizira m’bale wawo Saleh. Iye adati: 7:73 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:73) ayat 73 in Chichewa

7:73 Surah Al-A‘raf ayat 73 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 73 - الأعرَاف - Page - Juz 8

﴿وَإِلَىٰ ثَمُودَ أَخَاهُمۡ صَٰلِحٗاۚ قَالَ يَٰقَوۡمِ ٱعۡبُدُواْ ٱللَّهَ مَا لَكُم مِّنۡ إِلَٰهٍ غَيۡرُهُۥۖ قَدۡ جَآءَتۡكُم بَيِّنَةٞ مِّن رَّبِّكُمۡۖ هَٰذِهِۦ نَاقَةُ ٱللَّهِ لَكُمۡ ءَايَةٗۖ فَذَرُوهَا تَأۡكُلۡ فِيٓ أَرۡضِ ٱللَّهِۖ وَلَا تَمَسُّوهَا بِسُوٓءٖ فَيَأۡخُذَكُمۡ عَذَابٌ أَلِيمٞ ﴾
[الأعرَاف: 73]

Ndipo kwa anthu a Thamud, Ife tidawatumizira m’bale wawo Saleh. Iye adati: “Oh anthu anga! Pembedzani Mulungu. Inu mulibe mulungu wina koma Iye yekha. Ndithudi wadza umboni wokhulupirika kuchokera kwa Ambuye wanu. Iyi ndi Ngamira yaikazi ya Mulungu, chizindikiro kwa inu. Motero ilekeni kuti izidya m’dziko la Mulungu ndipo musaizunze ayi chifukwa mungapute chilango chowawa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإلى ثمود أخاهم صالحا قال ياقوم اعبدوا الله ما لكم من إله, باللغة نيانجا

﴿وإلى ثمود أخاهم صالحا قال ياقوم اعبدوا الله ما لكم من إله﴾ [الأعرَاف: 73]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo kwa Asamudu tidamtumiza m’bale wawo Swaleh. Adati: “E inu anthu anga! Gwadirani Allah; inu mulibe mulungu wina koma Iye basi. Chizindikiro chochokera kwa Mbuye wanu chadza kwa inu. Iyi ndi ngamira ya Allah monga chisonyezo chanu (chizizwa chanu), choncho, isiyeni izidya m’dziko la Allah, ndipo musaikhudze ndi choipa kuopera kuti chingakugwereni chilango chowawa kwambiri.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek