×

Motero Shaibu adawasiya iwo nati: “Oh inu anthu anga! Ndithudi ine ndidakuuzani 7:93 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-A‘raf ⮕ (7:93) ayat 93 in Chichewa

7:93 Surah Al-A‘raf ayat 93 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-A‘raf ayat 93 - الأعرَاف - Page - Juz 9

﴿فَتَوَلَّىٰ عَنۡهُمۡ وَقَالَ يَٰقَوۡمِ لَقَدۡ أَبۡلَغۡتُكُمۡ رِسَٰلَٰتِ رَبِّي وَنَصَحۡتُ لَكُمۡۖ فَكَيۡفَ ءَاسَىٰ عَلَىٰ قَوۡمٖ كَٰفِرِينَ ﴾
[الأعرَاف: 93]

Motero Shaibu adawasiya iwo nati: “Oh inu anthu anga! Ndithudi ine ndidakuuzani uthenga wa Ambuye wanga ndipo ndakupatsani ulangizi wabwino. Kodi ine ndingamvere bwanji chisoni anthu osakhulupirira?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فتولى عنهم وقال ياقوم لقد أبلغتكم رسالات ربي ونصحت لكم فكيف آسى, باللغة نيانجا

﴿فتولى عنهم وقال ياقوم لقد أبلغتكم رسالات ربي ونصحت لكم فكيف آسى﴾ [الأعرَاف: 93]

Khaled Ibrahim Betala
“(Pamene nthawi yakuonongeka kwawo idayandikira, Shuaib adatuluka m’mudzimo pamodzi ndi aja adakhulupirira) nawasiya oipawo (kunka kutali) uku akunena: “E inu anthu anga! Ndinafikitsadi uthenga wa Mbuye wanga ndipo ndinakuchenjezani ndiye nchotani ndidandaule za anthu okanira.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek