×

Ndidawauza: “Funsani chikhululukiro cha Ambuye wanu. Ndithudi Iye amakhululukira nthawi zonse.” 71:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Nuh ⮕ (71:10) ayat 10 in Chichewa

71:10 Surah Nuh ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Nuh ayat 10 - نُوح - Page - Juz 29

﴿فَقُلۡتُ ٱسۡتَغۡفِرُواْ رَبَّكُمۡ إِنَّهُۥ كَانَ غَفَّارٗا ﴾
[نُوح: 10]

Ndidawauza: “Funsani chikhululukiro cha Ambuye wanu. Ndithudi Iye amakhululukira nthawi zonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فقلت استغفروا ربكم إنه كان غفارا, باللغة نيانجا

﴿فقلت استغفروا ربكم إنه كان غفارا﴾ [نُوح: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho ndidati (kwa anthu anga): Pemphani kwa Mbuye wanu chikhululuko (pa kukana kwanu ndi kutonza kwanu), ndithu Iye ali Wokhululuka kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek