×

Motero Mulungu awapulumutsa iwo ku zoipa za tsiku limeneli ndi kuwapatsa nyali 76:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Insan ⮕ (76:11) ayat 11 in Chichewa

76:11 Surah Al-Insan ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 11 - الإنسَان - Page - Juz 29

﴿فَوَقَىٰهُمُ ٱللَّهُ شَرَّ ذَٰلِكَ ٱلۡيَوۡمِ وَلَقَّىٰهُمۡ نَضۡرَةٗ وَسُرُورٗا ﴾
[الإنسَان: 11]

Motero Mulungu awapulumutsa iwo ku zoipa za tsiku limeneli ndi kuwapatsa nyali yokongola kuti akhale mosavutika ndi mwachisangalalo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فوقاهم الله شر ذلك اليوم ولقاهم نضرة وسرورا, باللغة نيانجا

﴿فوقاهم الله شر ذلك اليوم ولقاهم نضرة وسرورا﴾ [الإنسَان: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo Allah adzawateteza mu mavuto a tsiku limenelo ndiponso adzawapatsa mtendere ndi chisangalalo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek