×

Iwo adzavala nsalu zokongola za silika zooneka ngati msipu zopetedwa ndi golide. 76:21 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Insan ⮕ (76:21) ayat 21 in Chichewa

76:21 Surah Al-Insan ayat 21 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 21 - الإنسَان - Page - Juz 29

﴿عَٰلِيَهُمۡ ثِيَابُ سُندُسٍ خُضۡرٞ وَإِسۡتَبۡرَقٞۖ وَحُلُّوٓاْ أَسَاوِرَ مِن فِضَّةٖ وَسَقَىٰهُمۡ رَبُّهُمۡ شَرَابٗا طَهُورًا ﴾
[الإنسَان: 21]

Iwo adzavala nsalu zokongola za silika zooneka ngati msipu zopetedwa ndi golide. Iwo adzavala zibangiri za siliva ndipo Ambuye wawo adzawapatsa chakumwa chabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: عاليهم ثياب سندس خضر وإستبرق وحلوا أساور من فضة وسقاهم ربهم شرابا, باللغة نيانجا

﴿عاليهم ثياب سندس خضر وإستبرق وحلوا أساور من فضة وسقاهم ربهم شرابا﴾ [الإنسَان: 21]

Khaled Ibrahim Betala
“Pamwamba pawo padzakhala nsalu zaveleveti zopyapyala, zobiriwira ndi nsalu zaveleveti zochindikala, akavekedwa m’manja mwawo zibangiri zasiliva; Mbuye wawo akawamwetsa chakumwa china choyera kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek