Quran with Chichewa translation - Surah Al-Insan ayat 24 - الإنسَان - Page - Juz 29
﴿فَٱصۡبِرۡ لِحُكۡمِ رَبِّكَ وَلَا تُطِعۡ مِنۡهُمۡ ءَاثِمًا أَوۡ كَفُورٗا ﴾
[الإنسَان: 24]
﴿فاصبر لحكم ربك ولا تطع منهم آثما أو كفورا﴾ [الإنسَان: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, pirira ndi lamulo la Mbuye wako ndipo usamvere wamachimo kapena wokanira aliyense mwa iwo |