×

Ndipo mverani Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo musatsutsane wina ndi mnzake chifukwa 8:46 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:46) ayat 46 in Chichewa

8:46 Surah Al-Anfal ayat 46 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 46 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَأَطِيعُواْ ٱللَّهَ وَرَسُولَهُۥ وَلَا تَنَٰزَعُواْ فَتَفۡشَلُواْ وَتَذۡهَبَ رِيحُكُمۡۖ وَٱصۡبِرُوٓاْۚ إِنَّ ٱللَّهَ مَعَ ٱلصَّٰبِرِينَ ﴾
[الأنفَال: 46]

Ndipo mverani Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo musatsutsane wina ndi mnzake chifukwa mudzakhumudwa ndi kuchita ulesi, ndipo pirirani. Ndithudi Mulungu ali pamodzi ndi anthu opirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأطيعوا الله ورسوله ولا تنازعوا فتفشلوا وتذهب ريحكم واصبروا إن الله مع, باللغة نيانجا

﴿وأطيعوا الله ورسوله ولا تنازعوا فتفشلوا وتذهب ريحكم واصبروا إن الله مع﴾ [الأنفَال: 46]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo mumvereni Allah ndi Mtumiki Wake, musakangane (kuopera kuti) mungakhale olephera (ndi kutaya mtima), ndikuchoka mphamvu zanu. Koma pitirizani kupirira. Ndithudi, Allah ali pamodzi ndi anthu opirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek