Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 55 - الأنفَال - Page - Juz 10
﴿إِنَّ شَرَّ ٱلدَّوَآبِّ عِندَ ٱللَّهِ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ فَهُمۡ لَا يُؤۡمِنُونَ ﴾ 
[الأنفَال: 55]
﴿إن شر الدواب عند الله الذين كفروا فهم لا يؤمنون﴾ [الأنفَال: 55]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndithu nyama zoipitsitsa kwa Allah ndi amene sakhulupirira. (amamkana Allah ngakhale choonadi akuchidziwa bwinobwino), choncho iwo sakhulupirira |