×

Monga anthu a Farawo ndi iwo amene adalipo kale, iwo sadakhulupirire uthenga 8:54 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:54) ayat 54 in Chichewa

8:54 Surah Al-Anfal ayat 54 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 54 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿كَدَأۡبِ ءَالِ فِرۡعَوۡنَ وَٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِمۡۚ كَذَّبُواْ بِـَٔايَٰتِ رَبِّهِمۡ فَأَهۡلَكۡنَٰهُم بِذُنُوبِهِمۡ وَأَغۡرَقۡنَآ ءَالَ فِرۡعَوۡنَۚ وَكُلّٞ كَانُواْ ظَٰلِمِينَ ﴾
[الأنفَال: 54]

Monga anthu a Farawo ndi iwo amene adalipo kale, iwo sadakhulupirire uthenga wa Ambuye wawo kotero Ife tidawaononga chifukwa cha zolakwa zawo ndipo Ife tidamiza anthu a Farawo chifukwa onse adali osalungama

❮ Previous Next ❯

ترجمة: كدأب آل فرعون والذين من قبلهم كذبوا بآيات ربهم فأهلكناهم بذنوبهم وأغرقنا, باللغة نيانجا

﴿كدأب آل فرعون والذين من قبلهم كذبوا بآيات ربهم فأهلكناهم بذنوبهم وأغرقنا﴾ [الأنفَال: 54]

Khaled Ibrahim Betala
“(Khalidwe lawo lili) ngati khalidwe la anthu a Farawo ndi omwe adalipo patsogolo pawo. Adatsutsa zizindikiro za Mbuye wawo. Choncho, tidawaononga chifukwa cha machimo awo, ndipo tidawamiza anthu a Farawo. Ndipo onse adali ochita zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek