×

Kutsutsana ndi iwe pa choonadi chimene chinadza ngati kuti iwo anali kuperekedwa 8:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:6) ayat 6 in Chichewa

8:6 Surah Al-Anfal ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 6 - الأنفَال - Page - Juz 9

﴿يُجَٰدِلُونَكَ فِي ٱلۡحَقِّ بَعۡدَ مَا تَبَيَّنَ كَأَنَّمَا يُسَاقُونَ إِلَى ٱلۡمَوۡتِ وَهُمۡ يَنظُرُونَ ﴾
[الأنفَال: 6]

Kutsutsana ndi iwe pa choonadi chimene chinadza ngati kuti iwo anali kuperekedwa ku imfa pamene iwo anali kuona

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يجادلونك في الحق بعد ما تبين كأنما يساقون إلى الموت وهم ينظرون, باللغة نيانجا

﴿يجادلونك في الحق بعد ما تبين كأنما يساقون إلى الموت وهم ينظرون﴾ [الأنفَال: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Akutsutsana nawe (pa chinthu) choona pambuyo pakuti chaonekera poyera. (Kukuwaipira kukumana ndi adani) ngati kuti akubusidwa kunka ku imfa akuona
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek