×

oh iwe Mtumwi! Alimbikitse anthu okhulupirira kuti amenye nkhondo. Ngati pali anthu 8:65 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:65) ayat 65 in Chichewa

8:65 Surah Al-Anfal ayat 65 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 65 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّبِيُّ حَرِّضِ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ عَلَى ٱلۡقِتَالِۚ إِن يَكُن مِّنكُمۡ عِشۡرُونَ صَٰبِرُونَ يَغۡلِبُواْ مِاْئَتَيۡنِۚ وَإِن يَكُن مِّنكُم مِّاْئَةٞ يَغۡلِبُوٓاْ أَلۡفٗا مِّنَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِأَنَّهُمۡ قَوۡمٞ لَّا يَفۡقَهُونَ ﴾
[الأنفَال: 65]

oh iwe Mtumwi! Alimbikitse anthu okhulupirira kuti amenye nkhondo. Ngati pali anthu makumi awiri opilira pakati panu, iwo adzagonjetsa anthu mazana awiri; ndipo ngati pali anthu zana limodzi, iwo adzagonjetsa anthu chikwi chimodzi cha anthu osakhulupirira chifukwa iwo ndi anthu amene sazindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها النبي حرض المؤمنين على القتال إن يكن منكم عشرون صابرون يغلبوا, باللغة نيانجا

﴿ياأيها النبي حرض المؤمنين على القتال إن يكن منكم عشرون صابرون يغلبوا﴾ [الأنفَال: 65]

Khaled Ibrahim Betala
“E iwe Mneneri! Alimbikitse okhulupirira kupita ku nkhondo. Ngati mwa inu muli anthu makumi awiri olimba mtima (ndiye kuti) adzawagonjetsa mazana awiri (a mwa anthu osakhulupirira). Ngati mwa inu muli anthu zana limodzi (olimba mtima ndiye kuti) adzagonjetsa chikwi chimodzi (1,000) cha anthu omwe sadakhulupirire, chifukwa chakuti iwo ndi anthu osazindikira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek