×

Ndithudi iwo amene adakhulupirira ndi kusamuka ndipoanapilirandikumenyankhondondichumachawondi iwoenim’njiraya Mulungundipondiiwoameneadawasunga ndi kuwathandiza, amenewa 8:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:72) ayat 72 in Chichewa

8:72 Surah Al-Anfal ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 72 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَهَاجَرُواْ وَجَٰهَدُواْ بِأَمۡوَٰلِهِمۡ وَأَنفُسِهِمۡ فِي سَبِيلِ ٱللَّهِ وَٱلَّذِينَ ءَاوَواْ وَّنَصَرُوٓاْ أُوْلَٰٓئِكَ بَعۡضُهُمۡ أَوۡلِيَآءُ بَعۡضٖۚ وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَلَمۡ يُهَاجِرُواْ مَا لَكُم مِّن وَلَٰيَتِهِم مِّن شَيۡءٍ حَتَّىٰ يُهَاجِرُواْۚ وَإِنِ ٱسۡتَنصَرُوكُمۡ فِي ٱلدِّينِ فَعَلَيۡكُمُ ٱلنَّصۡرُ إِلَّا عَلَىٰ قَوۡمِۭ بَيۡنَكُمۡ وَبَيۡنَهُم مِّيثَٰقٞۗ وَٱللَّهُ بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرٞ ﴾
[الأنفَال: 72]

Ndithudi iwo amene adakhulupirira ndi kusamuka ndipoanapilirandikumenyankhondondichumachawondi iwoenim’njiraya Mulungundipondiiwoameneadawasunga ndi kuwathandiza, amenewa adzakhala a bwenzi a wina ndi mnzake. Iwo amene akhulupirira koma sadasamuke mwa njira iliyonse iwe ulibe udindo pa iwo pokhapokha ngati iwo asamuka. Koma ngati iwo afuna chithandizo cha chipembedzo ndi udindo wako kuwathandiza kupatula anthu amene ali ndi pangano logwirizana pakati pa inu ndi iwo ndipo Mulungu amaona ntchito zanu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين آمنوا وهاجروا وجاهدوا بأموالهم وأنفسهم في سبيل الله والذين آووا, باللغة نيانجا

﴿إن الذين آمنوا وهاجروا وجاهدوا بأموالهم وأنفسهم في سبيل الله والذين آووا﴾ [الأنفَال: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu anthu amene anakhulupirira nasamuka kwawo ndi kumenyana pa njira ya Allah ndi chuma chawo ndi moyo wawo; ndiponso amene anawalandira (iwo) ndi kuwapatsa malo ndi kuwathandiza, awa ndiabale otchinjirizana wina ndi mnzake. Ndipo anthu amene akhulupirira koma nasiya kusamuka (kudza ku Madina), palibe udindo pa inu wa kuwateteza kufikira nawonso atasamuka (kudza ku Madina). Ngati atakupemphani chithandizo cha chipembedzo athandizeni, kupatula (akaputana ndi anthu) amene pakati panu ndi iwo pali chipangano, (pamenepo musawathandize pomenyana ndi osakhulupirirawo omwe muli nawo chipangano). Ndipo Allah Ngowoona zomwe muchita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek