×

Ndipo anthu osakhulupirira ndi abwenzi wina ndi mnzake. Ndipo ngati inu simuchita 8:73 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anfal ⮕ (8:73) ayat 73 in Chichewa

8:73 Surah Al-Anfal ayat 73 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 73 - الأنفَال - Page - Juz 10

﴿وَٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بَعۡضُهُمۡ أَوۡلِيَآءُ بَعۡضٍۚ إِلَّا تَفۡعَلُوهُ تَكُن فِتۡنَةٞ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَفَسَادٞ كَبِيرٞ ﴾
[الأنفَال: 73]

Ndipo anthu osakhulupirira ndi abwenzi wina ndi mnzake. Ndipo ngati inu simuchita chimodzimodzi mudzakhala chisokonezo ndi kuponderezana m’dziko ndiponso chionongeko chachikulu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين كفروا بعضهم أولياء بعض إلا تفعلوه تكن فتنة في الأرض وفساد, باللغة نيانجا

﴿والذين كفروا بعضهم أولياء بعض إلا تفعلوه تكن فتنة في الأرض وفساد﴾ [الأنفَال: 73]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (anthu) amene sadakhulupirire (Allah) amatetezana okha ndi kukhala abwenzi pakati pawo. Ngati nanunso simuchita izi, padzakhala chisokonezo m’dziko ndi chionongeko chachikulu
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek