Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anfal ayat 71 - الأنفَال - Page - Juz 10
﴿وَإِن يُرِيدُواْ خِيَانَتَكَ فَقَدۡ خَانُواْ ٱللَّهَ مِن قَبۡلُ فَأَمۡكَنَ مِنۡهُمۡۗ وَٱللَّهُ عَلِيمٌ حَكِيمٌ ﴾
[الأنفَال: 71]
﴿وإن يريدوا خيانتك فقد خانوا الله من قبل فأمكن منهم والله عليم﴾ [الأنفَال: 71]
Khaled Ibrahim Betala “Ngati akufuna kukuchitirani chinyengo (chinyengo chawo sichiphula kanthu pa iwe), ndithu anamuchitirapo kale Allah chinyengo (chifukwa cha kusakhulupirira kwawo). Choncho anakupatsa mphamvu zowagonjetsera iwo. Ndipo Allah Ngodziwa, Ngwanzeru zakuya |