×

Koma ngati iwo alapa, apitiliza mapemphero ndipo apereka msonkho wothandizira anthu osauka, 9:11 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:11) ayat 11 in Chichewa

9:11 Surah At-Taubah ayat 11 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 11 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿فَإِن تَابُواْ وَأَقَامُواْ ٱلصَّلَوٰةَ وَءَاتَوُاْ ٱلزَّكَوٰةَ فَإِخۡوَٰنُكُمۡ فِي ٱلدِّينِۗ وَنُفَصِّلُ ٱلۡأٓيَٰتِ لِقَوۡمٖ يَعۡلَمُونَ ﴾
[التوبَة: 11]

Koma ngati iwo alapa, apitiliza mapemphero ndipo apereka msonkho wothandizira anthu osauka, iwo ndiye kuti ndi abale anu m’chipembedzo. Ife timalongosola chivumbulutso mwatsatane tsatane kwa anthu ozindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فإن تابوا وأقاموا الصلاة وآتوا الزكاة فإخوانكم في الدين ونفصل الآيات لقوم, باللغة نيانجا

﴿فإن تابوا وأقاموا الصلاة وآتوا الزكاة فإخوانكم في الدين ونفصل الآيات لقوم﴾ [التوبَة: 11]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma ngati alapa nayamba kupemphera Swala ndikupereka chopereka (Zakaat), ndiye kuti ndi abale anu pa chipembedzo. Ndipo tikuzifotokoza Ayah zi (mwabwino) kwa anthu odziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek