Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 119 - التوبَة - Page - Juz 11
﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱتَّقُواْ ٱللَّهَ وَكُونُواْ مَعَ ٱلصَّٰدِقِينَ ﴾
[التوبَة: 119]
﴿ياأيها الذين آمنوا اتقوا الله وكونوا مع الصادقين﴾ [التوبَة: 119]
| Khaled Ibrahim Betala “E inu amene mwakhulupirira! Opani Allah, ndipo khalani pamodzi ndi owona (amene akuchitsimikiza Chisilamu chawo ndi zochita zawo, osati kungoyankhula pakamwa pokha) |