×

Iye adakhululukira anthu atatu amene adasiyidwa m’mbuyo, mpaka pamene kwa iwo dziko, 9:118 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:118) ayat 118 in Chichewa

9:118 Surah At-Taubah ayat 118 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 118 - التوبَة - Page - Juz 11

﴿وَعَلَى ٱلثَّلَٰثَةِ ٱلَّذِينَ خُلِّفُواْ حَتَّىٰٓ إِذَا ضَاقَتۡ عَلَيۡهِمُ ٱلۡأَرۡضُ بِمَا رَحُبَتۡ وَضَاقَتۡ عَلَيۡهِمۡ أَنفُسُهُمۡ وَظَنُّوٓاْ أَن لَّا مَلۡجَأَ مِنَ ٱللَّهِ إِلَّآ إِلَيۡهِ ثُمَّ تَابَ عَلَيۡهِمۡ لِيَتُوبُوٓاْۚ إِنَّ ٱللَّهَ هُوَ ٱلتَّوَّابُ ٱلرَّحِيمُ ﴾
[التوبَة: 118]

Iye adakhululukira anthu atatu amene adasiyidwa m’mbuyo, mpaka pamene kwa iwo dziko, ngakhale ndi lalikulu, linali lochepa ndipo mizimu yawo idapanikizika ndipo iwo adakhulupirira kuti kudalibe komuthawira Mulungu koma kupita kwa Iye. Motero Iye adavomera kulapa kwawo. Ndithudi Mulungu ndiye amene amavomera kulapa ndipo ndi wachisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وعلى الثلاثة الذين خلفوا حتى إذا ضاقت عليهم الأرض بما رحبت وضاقت, باللغة نيانجا

﴿وعلى الثلاثة الذين خلفوا حتى إذا ضاقت عليهم الأرض بما رحبت وضاقت﴾ [التوبَة: 118]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndiponso (adawatembenukira mwachifundo) aja atatu amene adawadikiritsa (pakusavomera msanga kulapa kwawo), kufikira pamene dziko lidawapana ngakhale lidali lophanuka, nabanika m’mitima mwawo natsimikiza kuti palibe komuthawira Allah (kwina) koma kwa Iye (Allah polapa). Kenako (Allah) adawatsogolera kulapa kuti alape. Ndithu Allah Ngolandira kulapa, Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek