Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 25 - التوبَة - Page - Juz 10
﴿لَقَدۡ نَصَرَكُمُ ٱللَّهُ فِي مَوَاطِنَ كَثِيرَةٖ وَيَوۡمَ حُنَيۡنٍ إِذۡ أَعۡجَبَتۡكُمۡ كَثۡرَتُكُمۡ فَلَمۡ تُغۡنِ عَنكُمۡ شَيۡـٔٗا وَضَاقَتۡ عَلَيۡكُمُ ٱلۡأَرۡضُ بِمَا رَحُبَتۡ ثُمَّ وَلَّيۡتُم مُّدۡبِرِينَ ﴾
[التوبَة: 25]
﴿لقد نصركم الله في مواطن كثيرة ويوم حنين إذ أعجبتكم كثرتكم فلم﴾ [التوبَة: 25]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu Allah wakhala akukupulumutsani (kwa adani anu) m’malo ambiri omenyanira nkhondo, ndi pa tsiku la Hunaini, pamene kudakunyengani kuchuluka kwanu. Koma sikudakuthandizeni chilichonse. Ndipo dziko lidakupanani ngakhale kuti lidali lotambasuka ndipo kenako mudatembenukira kumbuyo (kuthawa) |