×

Ndipo Mulungu adatsitsa chisomo chake pa Mtumwi wakendikwaokhulupirirandipoadatumizaAsirikaliamene inu simudawaone ndipo analanga 9:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah At-Taubah ⮕ (9:26) ayat 26 in Chichewa

9:26 Surah At-Taubah ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah At-Taubah ayat 26 - التوبَة - Page - Juz 10

﴿ثُمَّ أَنزَلَ ٱللَّهُ سَكِينَتَهُۥ عَلَىٰ رَسُولِهِۦ وَعَلَى ٱلۡمُؤۡمِنِينَ وَأَنزَلَ جُنُودٗا لَّمۡ تَرَوۡهَا وَعَذَّبَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْۚ وَذَٰلِكَ جَزَآءُ ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[التوبَة: 26]

Ndipo Mulungu adatsitsa chisomo chake pa Mtumwi wakendikwaokhulupirirandipoadatumizaAsirikaliamene inu simudawaone ndipo analanga anthu osakhulupirira. Amenewa ndiwo malipiro a anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ثم أنـزل الله سكينته على رسوله وعلى المؤمنين وأنـزل جنودا لم تروها, باللغة نيانجا

﴿ثم أنـزل الله سكينته على رسوله وعلى المؤمنين وأنـزل جنودا لم تروها﴾ [التوبَة: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“Kenaka Allah adatsitsa mpumulo Wake kwa Mtumiki Wake ndi kwa okhulupirira. Ndipo adatsitsa asilikali ankhondo (angelo) omwe simudawaone. Ndipo adawakhaulitsa osakhulupirira. Imeneyo ndiyo mphoto ya osakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek