Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shams ayat 8 - الشَّمس - Page - Juz 30
﴿فَأَلۡهَمَهَا فُجُورَهَا وَتَقۡوَىٰهَا ﴾
[الشَّمس: 8]
﴿فألهمها فجورها وتقواها﴾ [الشَّمس: 8]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adaudziwitsa zoipa zake ndi zabwino zake; (ndi kuwupatsa ufulu ndi mphamvu zochitira zimene ukufuna) |