Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 101 - يُونس - Page - Juz 11
﴿قُلِ ٱنظُرُواْ مَاذَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۚ وَمَا تُغۡنِي ٱلۡأٓيَٰتُ وَٱلنُّذُرُ عَن قَوۡمٖ لَّا يُؤۡمِنُونَ ﴾
[يُونس: 101]
﴿قل انظروا ماذا في السموات والأرض وما تغني الآيات والنذر عن قوم﴾ [يُونس: 101]
Khaled Ibrahim Betala “Nena: “Yang’anani nchiyani chikupezeka kumwamba ndi pansi!” Ndipo zisonyezo zonsezi ndi machenjezo onsewa sangawakwanire (ndi kuwapindulira kanthu) anthu osakhulupirira |