×

Nena, “Mulungu akadafuna, ine sindikadawerengailokwainundiponsoIyesakadakupatsani inu nzeru zoti mulidziwe. Ndithu moyo wanga 10:16 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Yunus ⮕ (10:16) ayat 16 in Chichewa

10:16 Surah Yunus ayat 16 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Yunus ayat 16 - يُونس - Page - Juz 11

﴿قُل لَّوۡ شَآءَ ٱللَّهُ مَا تَلَوۡتُهُۥ عَلَيۡكُمۡ وَلَآ أَدۡرَىٰكُم بِهِۦۖ فَقَدۡ لَبِثۡتُ فِيكُمۡ عُمُرٗا مِّن قَبۡلِهِۦٓۚ أَفَلَا تَعۡقِلُونَ ﴾
[يُونس: 16]

Nena, “Mulungu akadafuna, ine sindikadawerengailokwainundiponsoIyesakadakupatsani inu nzeru zoti mulidziwe. Ndithu moyo wanga wonse ndakhala ndili pakati panu, Bukuli lisadavumbulutsidwe. Kodi simungathe kuzindikira?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل لو شاء الله ما تلوته عليكم ولا أدراكم به فقد لبثت, باللغة نيانجا

﴿قل لو شاء الله ما تلوته عليكم ولا أدراكم به فقد لبثت﴾ [يُونس: 16]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Allah akadafuna, sindikadakuwerengerani Qur’aniyi ndiponso sakadakudziwitsani Qur’aniyo, ndidakhala pakati panu moyo wanga (zaka zambiri) isadavumbulutsidwe, (simudandimve ndikunena chilichonse cha utumiki). Kodi mulibe nzeru?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek